Mateyu 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo atamumanga, anapita kukamupereka kwa Bwanamkubwa Pilato.+ Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula.
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula.