Ekisodo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye ananenanso kuti: “Ndine Mulungu wa makolo* ako, Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo.”+ Atatero Mose anaphimba nkhope yake chifukwa ankaopa kuyangʼana Mulungu woona.
6 Iye ananenanso kuti: “Ndine Mulungu wa makolo* ako, Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo.”+ Atatero Mose anaphimba nkhope yake chifukwa ankaopa kuyangʼana Mulungu woona.