Mateyu 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zimene zinachitika kuti Yesu Khristu abadwe ndi izi: Pa nthawi imene mayi ake Mariya anali atalonjezedwa ndi Yosefe kuti adzamukwatira, Mariyayo anapezeka kuti ndi woyembekezera mwa mzimu woyera*+ asanakwatirane.
18 Zimene zinachitika kuti Yesu Khristu abadwe ndi izi: Pa nthawi imene mayi ake Mariya anali atalonjezedwa ndi Yosefe kuti adzamukwatira, Mariyayo anapezeka kuti ndi woyembekezera mwa mzimu woyera*+ asanakwatirane.