Mateyu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu wanu ubwere.+ Zofuna zanu+ zichitike padziko lapansi pano ngati mmene zilili kumwamba.+ Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+ Maliko 14:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako anati: “Abba,* Atate,+ zinthu zonse nʼzotheka kwa inu. Ndichotsereni kapu iyi. Komatu osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+ Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chimene ndangoganiza pandekha. Ndimaweruza mogwirizana ndi zimene ndamva, ndipo chiweruzo changa nʼcholungama,+ chifukwa sindichita zofuna zanga, koma zofuna za amene anandituma.+ Yohane 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chifukwa ndinabwera kuchokera kumwamba+ kudzachita zofuna za amene anandituma, osati zofuna zanga.+
39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+
36 Kenako anati: “Abba,* Atate,+ zinthu zonse nʼzotheka kwa inu. Ndichotsereni kapu iyi. Komatu osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+
30 Ine sindingachite chilichonse chimene ndangoganiza pandekha. Ndimaweruza mogwirizana ndi zimene ndamva, ndipo chiweruzo changa nʼcholungama,+ chifukwa sindichita zofuna zanga, koma zofuna za amene anandituma.+
38 Chifukwa ndinabwera kuchokera kumwamba+ kudzachita zofuna za amene anandituma, osati zofuna zanga.+