Yohane 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “Apachikidwe ameneyo! Apachikidwe ameneyo!”*+ Pilato anawauza kuti: “Mutengeni mukamupachike nokha,* chifukwa ine sindinamupeze ndi mlandu uliwonse.”+
6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “Apachikidwe ameneyo! Apachikidwe ameneyo!”*+ Pilato anawauza kuti: “Mutengeni mukamupachike nokha,* chifukwa ine sindinamupeze ndi mlandu uliwonse.”+