Agalatiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholinga chake chinali chakuti kudzera mwa Khristu Yesu, mitundu ya anthu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.
14 Cholinga chake chinali chakuti kudzera mwa Khristu Yesu, mitundu ya anthu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.