-
Aefeso 5:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chifukwa mfundo iyi mukuidziwa ndipo mukuimvetsa bwino, kuti munthu wachiwerewere*+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndi kulambira mafano, sadzalowa mu Ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+
6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake, chifukwa mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a osamvera, amene akuchita zinthu zimene ndatchulazi.
-