-
Machitidwe 15:28, 29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Chifukwa mzimu woyera+ komanso ifeyo taona kuti ndi bwino kuti tisakusenzetseni mtolo wolemera, kupatula zinthu zofunika zokhazi zomwe ndi 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola*+ ndi chiwerewere.*+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri, zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”*
-