-
Numeri 21:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Upange chifanizo cha njoka yapoizoni* ndipo uchiike pamtengo. Ndiye munthu aliyense akalumidwa, aziyangʼana chifanizocho kuti akhalebe ndi moyo.” 9 Nthawi yomweyo Mose anapanga njoka yakopa+ nʼkuiika pamtengo.+ Ndiye munthu akalumidwa ndi njoka nʼkuyangʼana njoka yakopayo, ankakhalabe ndi moyo.+
-