Machitidwe 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Paulo anati: “Ubatizo umene Yohane ankabatiza anthu unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Ankauza anthu kuti akhulupirire amene akubwera mʼmbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”
4 Kenako Paulo anati: “Ubatizo umene Yohane ankabatiza anthu unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Ankauza anthu kuti akhulupirire amene akubwera mʼmbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”