Mateyu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndikukubatizani mʼmadzi chifukwa chakuti mwalapa,+ koma amene akubwera mʼmbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.*+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso moto.+ Maliko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yohane Mʼbatizi anali mʼchipululu ndipo ankalalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+
11 Ine ndikukubatizani mʼmadzi chifukwa chakuti mwalapa,+ koma amene akubwera mʼmbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.*+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso moto.+
4 Yohane Mʼbatizi anali mʼchipululu ndipo ankalalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+