Mateyu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndikukubatizani mʼmadzi chifukwa chakuti mwalapa,+ koma amene akubwera mʼmbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.*+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso moto.+ Machitidwe 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Yohane ankabatiza ndi madzi, koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera+ pasanathe masiku ambiri.” Machitidwe 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano onse anali atasonkhana pamodzi pa tsiku la Chikondwerero cha Pentekosite.+ Machitidwe 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+
11 Ine ndikukubatizani mʼmadzi chifukwa chakuti mwalapa,+ koma amene akubwera mʼmbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.*+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso moto.+
5 Chifukwa Yohane ankabatiza ndi madzi, koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera+ pasanathe masiku ambiri.”
4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+