Mateyu 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine+ ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha.+ Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+
27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine+ ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha.+ Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+