Machitidwe 9:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ali pa ulendo wakewo, atatsala pangʼono kufika ku Damasiko, mwadzidzidzi anangoona kuwala kochokera kumwamba kutamuzungulira.+ 4 Zitatero anagwa pansi ndipo anamva mawu akuti: “Saulo, Saulo, nʼchifukwa chiyani ukundizunza?” 1 Akorinto 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi ndilibe ufulu wochita zimene ndikufuna? Kodi si ine mtumwi? Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu?+ Kodi inu si ntchito yanga mwa Ambuye?
3 Ali pa ulendo wakewo, atatsala pangʼono kufika ku Damasiko, mwadzidzidzi anangoona kuwala kochokera kumwamba kutamuzungulira.+ 4 Zitatero anagwa pansi ndipo anamva mawu akuti: “Saulo, Saulo, nʼchifukwa chiyani ukundizunza?”
9 Kodi ndilibe ufulu wochita zimene ndikufuna? Kodi si ine mtumwi? Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu?+ Kodi inu si ntchito yanga mwa Ambuye?