Machitidwe 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera akumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena, 1 Akorinto 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu akumanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena akuti, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso akuti, “Ine ndine wa Kefa,”* pamene ena akuti, “Ine ndine wa Khristu.” 1 Akorinto 3:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi Apolo ndi ndani? Nanga Paulo ndi ndani? Ife tangokhala atumiki+ amene tinakuthandizani kukhala okhulupirira, mogwirizana ndi ntchito imene Ambuye anatipatsa. 6 Ineyo ndinadzala,+ Apolo anathirira,+ koma Mulungu ndi amene anakulitsa.
19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera akumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena,
12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu akumanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena akuti, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso akuti, “Ine ndine wa Kefa,”* pamene ena akuti, “Ine ndine wa Khristu.”
5 Kodi Apolo ndi ndani? Nanga Paulo ndi ndani? Ife tangokhala atumiki+ amene tinakuthandizani kukhala okhulupirira, mogwirizana ndi ntchito imene Ambuye anatipatsa. 6 Ineyo ndinadzala,+ Apolo anathirira,+ koma Mulungu ndi amene anakulitsa.