Machitidwe 11:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa nthawiyi, aneneri+ ochokera ku Yerusalemu anapita ku Antiokeya. 28 Mothandizidwa ndi mzimu wa Mulungu, mmodzi wa iwo dzina lake Agabo,+ analosera kuti padziko lonse lapansi+ padzagwa njala yaikulu. Izi zinachitikadi mʼnthawi ya Kalaudiyo.
27 Pa nthawiyi, aneneri+ ochokera ku Yerusalemu anapita ku Antiokeya. 28 Mothandizidwa ndi mzimu wa Mulungu, mmodzi wa iwo dzina lake Agabo,+ analosera kuti padziko lonse lapansi+ padzagwa njala yaikulu. Izi zinachitikadi mʼnthawi ya Kalaudiyo.