-
Luka 24:46-48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 ndipo anawauza kuti, “Malemba amanena kuti: Khristu adzazunzika ndipo tsiku lachitatu adzauka kwa akufa,+ 47 ndipo mʼdzina lake, uthenga woti anthu alape machimo awo+ kuti akhululukidwe udzalalikidwa kwa anthu a mitundu yonse,+ kuyambira ku Yerusalemu.+ 48 Inu mudzakhala mboni za zinthu zimenezi.+
-