Machitidwe 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Mulungu anamuukitsa+ pomumasula ku zopweteka* za imfa, chifukwa zinali zosatheka kuti imfa imugwire mwamphamvu.+ Machitidwe 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Mulungu anamuukitsa.+ 1 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kudzera mwa iye, mukukhulupirira Mulungu+ amene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumupatsa ulemerero,+ nʼcholinga choti chikhulupiriro ndiponso chiyembekezo chanu zikhale mwa Mulungu.
24 Koma Mulungu anamuukitsa+ pomumasula ku zopweteka* za imfa, chifukwa zinali zosatheka kuti imfa imugwire mwamphamvu.+
21 Kudzera mwa iye, mukukhulupirira Mulungu+ amene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumupatsa ulemerero,+ nʼcholinga choti chikhulupiriro ndiponso chiyembekezo chanu zikhale mwa Mulungu.