4 Aliyense wa inu azidziwa kulamulira thupi lake+ kuti likhale loyera+ komanso lolemekezeka pamaso pa Mulungu. 5 Musakhale ngati anthu a mitundu ina omwe sadziwa Mulungu+ komanso ali ndi chilakolako chosalamulirika cha kugonana+ ndipo sakhutiritsidwa.