-
Aroma 5:3-5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Si zokhazo, koma tikhozanso kumasangalala* tikakumana ndi mavuto+ chifukwa tikudziwa kuti mavuto athu amachititsa kuti tipirire.+ 4 Kupirira kumachititsa kuti tikhale ovomerezeka kwa Mulungu+ ndipo kukhala ovomerezeka kwa Mulungu kumachititsa kuti tikhale ndi chiyembekezo.+ 5 Chiyembekezocho sichitikhumudwitsa+ chifukwa Mulungu amasonyeza kuti amatikonda pogwiritsa ntchito mzimu woyera umene amatipatsa.+
-