Machitidwe 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anakwiya chifukwa atumwiwo ankaphunzitsa anthu ndiponso kulalikira mosapita mʼmbali zoti Yesu anaukitsidwa.+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+
2 Iwo anakwiya chifukwa atumwiwo ankaphunzitsa anthu ndiponso kulalikira mosapita mʼmbali zoti Yesu anaukitsidwa.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+