Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah) 1 Yohane 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, choncho tikavomereza machimo athu, adzatikhululukira komanso kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah)
9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, choncho tikavomereza machimo athu, adzatikhululukira komanso kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+