Aefeso 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene Mulunguyo anaugwiritsa ntchito pokuikani chidindo+ kuti mudzamasulidwe ndi dipo+ pa tsiku lachipulumutso.
30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene Mulunguyo anaugwiritsa ntchito pokuikani chidindo+ kuti mudzamasulidwe ndi dipo+ pa tsiku lachipulumutso.