Aroma 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za thupi.+ Koma otsatira mzimu, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za mzimu.+ Yakobo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Imeneyi si nzeru yochokera kumwamba, koma ndi yapadziko lapansi,+ yauchinyama ndiponso yauchiwanda.
5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za thupi.+ Koma otsatira mzimu, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za mzimu.+
15 Imeneyi si nzeru yochokera kumwamba, koma ndi yapadziko lapansi,+ yauchinyama ndiponso yauchiwanda.