1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu zamʼdziko* savomereza* zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa, chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu. Afilipi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu amenewo akuyembekezera kuwonongedwa ndipo mulungu wawo ndi mimba zawo. Iwo amanyadira zinthu zimene akuyenera kuchita nazo manyazi ndipo amangoganizira zinthu zapadziko lapansi.+
14 Koma munthu wokonda zinthu zamʼdziko* savomereza* zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa, chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
19 Anthu amenewo akuyembekezera kuwonongedwa ndipo mulungu wawo ndi mimba zawo. Iwo amanyadira zinthu zimene akuyenera kuchita nazo manyazi ndipo amangoganizira zinthu zapadziko lapansi.+