1 Timoteyo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso amangokhala osachita kanthu nʼkumangoyendayenda mʼmakomo mwa anzawo. Kuwonjezera pa kumangokhala osachita kanthu, amakondanso miseche, kulowerera nkhani za eni+ komanso kulankhula zinthu zimene sayenera kulankhula. 1 Petulo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma sindikufuna kuti wina wa inu azivutika chifukwa choti wayamba kuba, kupha anthu, kuchita zoipa kapena chifukwa choti akulowerera nkhani za eni.+
13 Komanso amangokhala osachita kanthu nʼkumangoyendayenda mʼmakomo mwa anzawo. Kuwonjezera pa kumangokhala osachita kanthu, amakondanso miseche, kulowerera nkhani za eni+ komanso kulankhula zinthu zimene sayenera kulankhula.
15 Koma sindikufuna kuti wina wa inu azivutika chifukwa choti wayamba kuba, kupha anthu, kuchita zoipa kapena chifukwa choti akulowerera nkhani za eni.+