-
Machitidwe 6:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Anthu onsewo anasangalala ndi mawu amenewa moti anasankha Sitefano, munthu wa chikhulupiriro cholimba ndiponso wodzaza ndi mzimu woyera. Anasankhanso Filipo,+ Purokoro, Nikanora, Timoni, Paremena ndi Nikolao wa ku Antiokeya amene analowa Chiyuda. 6 Ndiyeno anawabweretsa kwa atumwi, ndipo atapemphera, atumwiwo anawagwira pamutu* posonyeza kuti awapatsa udindo.+
-