Mlaliki 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso Mulungu woona akapatsa munthu chuma ndiponso zinthu zambiri+ zimene angathe kusangalala nazo, ayenera kulandira mphoto yake* ndi kusangalala chifukwa cha ntchito imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+ Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho nthawi zonse muziika Ufumu ndi mfundo zolungama za Mulungu pamalo oyamba pa moyo wanu, ndipo iye adzakupatsani zinthu zina zonsezi.+ Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+
19 Komanso Mulungu woona akapatsa munthu chuma ndiponso zinthu zambiri+ zimene angathe kusangalala nazo, ayenera kulandira mphoto yake* ndi kusangalala chifukwa cha ntchito imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+
33 Choncho nthawi zonse muziika Ufumu ndi mfundo zolungama za Mulungu pamalo oyamba pa moyo wanu, ndipo iye adzakupatsani zinthu zina zonsezi.+
17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+