Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+ 1 Petulo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wetani gulu la nkhosa za Mulungu+ zomwe zili mʼmanja mwanu. Monga oyangʼanira, muzigwira ntchito yanu, osati mokakamizika koma mofunitsitsa monga atumiki a Mulungu.+ Muziigwira ndi mtima wonse, osati chifukwa chofuna kupindulapo kenakake.+
5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+
2 Wetani gulu la nkhosa za Mulungu+ zomwe zili mʼmanja mwanu. Monga oyangʼanira, muzigwira ntchito yanu, osati mokakamizika koma mofunitsitsa monga atumiki a Mulungu.+ Muziigwira ndi mtima wonse, osati chifukwa chofuna kupindulapo kenakake.+