Aefeso 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anatisankha kuti tikakhale ogwirizana ndi Khristu dziko lisanakhazikitsidwe nʼcholinga choti tizisonyeza chikondi komanso kuti tikhale oyera ndiponso opanda chilema+ pamaso pa Mulungu. Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho, abale athu oyera, amene muli mʼgulu la anthu oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
4 Iye anatisankha kuti tikakhale ogwirizana ndi Khristu dziko lisanakhazikitsidwe nʼcholinga choti tizisonyeza chikondi komanso kuti tikhale oyera ndiponso opanda chilema+ pamaso pa Mulungu.
3 Choncho, abale athu oyera, amene muli mʼgulu la anthu oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+