1 Akorinto 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Payeneradi kukhala magulu ampatuko pakati panu,+ kuti anthu ovomerezeka kwa Mulungu adziwike. Chivumbulutso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, pali chinthu chimodzi chimene ukuchita bwino: Umadana ndi zochita za mpatuko wa Nikolao,+ zimenenso ine ndimadana nazo.
6 Komabe, pali chinthu chimodzi chimene ukuchita bwino: Umadana ndi zochita za mpatuko wa Nikolao,+ zimenenso ine ndimadana nazo.