-
Akolose 4:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Epafura,+ amene anachokera pakati panu, kapolo wa Khristu Yesu, akuti moni. Iye amakupemphererani mwakhama nthawi zonse kuti mupitirize kukhala olimba mwauzimu komanso kuti musamakayikire ngakhale pangʼono zinthu zonse zimene Mulungu adzachite. 13 Ndikumuchitiradi umboni kuti amadzipereka kwambiri chifukwa cha inu komanso chifukwa cha abale a ku Laodikaya ndi ku Herapoli.
-