Akolose 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Epafura,+ amene anachokera pakati panu, kapolo wa Khristu Yesu, akuti moni. Iye amakupemphererani mwakhama nthawi zonse, kuti pomalizira pake mukhale okhwima mwauzimu+ ndi osakayika ngakhale pang’ono za chifuniro chonse cha Mulungu. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:12 Nsanja ya Olonda,2/15/2008, ptsa. 3-412/15/2000, ptsa. 15-16, 19-245/15/1997, tsa. 31
12 Epafura,+ amene anachokera pakati panu, kapolo wa Khristu Yesu, akuti moni. Iye amakupemphererani mwakhama nthawi zonse, kuti pomalizira pake mukhale okhwima mwauzimu+ ndi osakayika ngakhale pang’ono za chifuniro chonse cha Mulungu.