Ekisodo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+ Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?” Yeremiya 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka mʼdziko la Iguputo mpaka pano.+ Choncho ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse omwe ndi aneneri, ndinkawatumiza tsiku lililonse, mobwerezabwereza.*+
3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+
8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”
25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka mʼdziko la Iguputo mpaka pano.+ Choncho ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse omwe ndi aneneri, ndinkawatumiza tsiku lililonse, mobwerezabwereza.*+