Luka 22:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma anazunzika koopsa mumtima mwake, moti anapitiriza kupemphera ndi mtima wonse+ ndipo thukuta lake linkaoneka ngati madontho amagazi amene akugwera pansi. Yohane 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera.
44 Koma anazunzika koopsa mumtima mwake, moti anapitiriza kupemphera ndi mtima wonse+ ndipo thukuta lake linkaoneka ngati madontho amagazi amene akugwera pansi.
27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera.