13 Ndithudi, nʼchifukwa chake ifenso timathokoza Mulungu mosalekeza,+ chifukwa pamene munalandira mawu a Mulungu amene munamva kwa ife, simunawalandire monga mawu a anthu, koma mmene alilidi, monga mawu a Mulungu. Mawu amenewa akugwiranso ntchito mwa inu okhulupirira.