21 Ndiyeno Yehova anayamba kumva fungo losangalatsa. Choncho Yehova ananena mumtima mwake kuti: “Sindidzatembereranso nthaka+ chifukwa cha zochita za anthu, popeza maganizo a anthu amakhala oipa kuyambira ali ana.+ Ndipo sindidzaphanso chamoyo chilichonse ngati mmene ndachitiramu.+