Mateyu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa kudzabwera anthu onamizira kuti ndi Khristu komanso aneneri abodza+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu ndiponso zodabwitsa, kuti ngati nʼkotheka, adzasocheretse+ ngakhale osankhidwawo. Aefeso 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho tisakhalenso ana. Tisamatengeketengeke ngati kuti tikukankhidwa ndi mafunde ndiponso tisamatengeke kupita uku ndi uku ndi mphepo iliyonse ya zinthu zachinyengo zimene anthu amaphunzitsa+ popeka mabodza mochenjera.
24 Chifukwa kudzabwera anthu onamizira kuti ndi Khristu komanso aneneri abodza+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu ndiponso zodabwitsa, kuti ngati nʼkotheka, adzasocheretse+ ngakhale osankhidwawo.
14 Choncho tisakhalenso ana. Tisamatengeketengeke ngati kuti tikukankhidwa ndi mafunde ndiponso tisamatengeke kupita uku ndi uku ndi mphepo iliyonse ya zinthu zachinyengo zimene anthu amaphunzitsa+ popeka mabodza mochenjera.