Agalatiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abale, ngati munthu wapatuka nʼkuyamba kulowera njira yolakwika mosazindikira, inu amene ndi oyenerera mwauzimu, yesani kuthandiza munthu woteroyo ndi mzimu wofatsa.+ Koma pamene mukuchita zimenezi musamale,+ kuopera kuti inunso mungayesedwe.+ Yakobo 5:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga, ngati wina pakati panu wasiya choonadi chifukwa chosocheretsedwa, ndiye munthu wina nʼkumubweza, 20 dziwani kuti amene wabweza wochimwayo panjira yake yoipa,+ wamupulumutsa ku imfa ndipo Mulungu adzakhululukira wochimwayo machimo ambiri.+
6 Abale, ngati munthu wapatuka nʼkuyamba kulowera njira yolakwika mosazindikira, inu amene ndi oyenerera mwauzimu, yesani kuthandiza munthu woteroyo ndi mzimu wofatsa.+ Koma pamene mukuchita zimenezi musamale,+ kuopera kuti inunso mungayesedwe.+
19 Abale anga, ngati wina pakati panu wasiya choonadi chifukwa chosocheretsedwa, ndiye munthu wina nʼkumubweza, 20 dziwani kuti amene wabweza wochimwayo panjira yake yoipa,+ wamupulumutsa ku imfa ndipo Mulungu adzakhululukira wochimwayo machimo ambiri.+