Chivumbulutso 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atamatula chidindo chachitatu,+ ndinamva mngelo wachitatu+ akunena kuti: “Bwera!” Ndipo nditayangʼana, ndinaona hatchi yakuda. Amene anakwera pahatchiyo anali ndi sikelo mʼdzanja lake.
5 Atamatula chidindo chachitatu,+ ndinamva mngelo wachitatu+ akunena kuti: “Bwera!” Ndipo nditayangʼana, ndinaona hatchi yakuda. Amene anakwera pahatchiyo anali ndi sikelo mʼdzanja lake.