Chivumbulutso 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo woyamba ankaoneka ngati mkango.+ Mngelo wachiwiri ankaoneka ngati mwana wa ngʼombe wamphongo.+ Mngelo wachitatu+ anali ndi nkhope yooneka ngati ya munthu ndipo mngelo wa 4+ ankaoneka ngati chiwombankhanga chimene chikuuluka.+
7 Mngelo woyamba ankaoneka ngati mkango.+ Mngelo wachiwiri ankaoneka ngati mwana wa ngʼombe wamphongo.+ Mngelo wachitatu+ anali ndi nkhope yooneka ngati ya munthu ndipo mngelo wa 4+ ankaoneka ngati chiwombankhanga chimene chikuuluka.+