Mateyu 17:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi mchimwene wake Yohane nʼkukwera nawo mʼphiri lalitali kwaokhaokha.+ 2 Ndiyeno iwo anaona kuti wasintha maonekedwe ake. Nkhope yake inawala ngati dzuwa ndipo malaya ake akunja anawala* kwambiri.+
17 Patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi mchimwene wake Yohane nʼkukwera nawo mʼphiri lalitali kwaokhaokha.+ 2 Ndiyeno iwo anaona kuti wasintha maonekedwe ake. Nkhope yake inawala ngati dzuwa ndipo malaya ake akunja anawala* kwambiri.+