Chivumbulutso 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akulu 24 aja+ ankagwada nʼkuwerama pamaso pa Amene wakhala pampando wachifumuyo, nʼkulambira Amene adzakhale ndi moyo kwamuyayayo. Iwo ankaponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo nʼkunena kuti:
10 akulu 24 aja+ ankagwada nʼkuwerama pamaso pa Amene wakhala pampando wachifumuyo, nʼkulambira Amene adzakhale ndi moyo kwamuyayayo. Iwo ankaponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo nʼkunena kuti: