9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ imene imadziwika kuti Mdyerekezi+ komanso Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi kumene kuli anthu.+ Iye anaponyedwa padziko lapansi+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.