Chivumbulutso 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo amene ziwanda zimakhala. Wakhalanso malo amene mzimu uliwonse wonyansa* komanso mbalame iliyonse yonyansa ndi imene imadedwa zimabisala.+
2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo amene ziwanda zimakhala. Wakhalanso malo amene mzimu uliwonse wonyansa* komanso mbalame iliyonse yonyansa ndi imene imadedwa zimabisala.+