-
Chivumbulutso 2:26, 27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndipo amene wapambana pankhondo nʼkumatsatira ntchito zanga mpaka mapeto, ndidzamupatsa ulamuliro pa mitundu ya anthu.+ 27 Ulamuliro wake udzakhala wofanana ndi umene ine ndalandira kuchokera kwa Atate wanga. Iye adzakusa anthu ndi ndodo yachitsulo+ moti anthuwo adzaphwanyidwaphwanyidwa ngati mbiya zadothi.
-