Chivumbulutso 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iyeyo adzakusa anthu ndi ndodo yachitsulo,+ ngati imenenso ine ndailandira kwa Atate wanga. Anthuwo adzaphwanyidwaphwanyidwa ngati mbiya zadothi.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:27 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 53, 281 Nsanja ya Olonda,8/15/1990, tsa. 31
27 Iyeyo adzakusa anthu ndi ndodo yachitsulo,+ ngati imenenso ine ndailandira kwa Atate wanga. Anthuwo adzaphwanyidwaphwanyidwa ngati mbiya zadothi.+