December 30, 2019–January 5, 2020
CHIVUMBULUTSO 20-22
Nyimbo Na. 146 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”: (10 min.)
Chiv. 21:1—“Kumwamba kwakale ndi dziko lapansi lakale zinali zitachoka” (re 301 ¶2)
Chiv. 21:3, 4—“Zakalezo zapita” (w13 12/1 11 ¶2-4)
Chiv. 21:5—Malonjezo a Yehova ndi odalirika (w03 8/1 12 ¶14)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Chiv. 20:5—Kodi “Akufa enawo” adzakhala bwanji ndi moyo kumapeto kwa zaka 1,000? (it-2 249 ¶2)
Chiv. 20:14, 15—Kodi “Nyanja yamoto” ikuimira chiyani? (it-2 189-190)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 20:1-15 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 4 min.) Sankhani lemba lililonse. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 9)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) jl phunziro 12 (th phunziro 6)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzisintha Ulaliki Wanu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 66
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 94 ndi Pemphero