December Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya December 2019 Zimene Tinganene December 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 7-9 Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova December 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 10-12 “Mboni Ziwiri” Zinaphedwa Koma Zinakhalanso ndi Moyo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Dziko “Linameza Mtsinje” December 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 13-16 Musamaope Zilombo Zoopsa December 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 17-19 Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse December 30, 2019–January 5, 2020 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 20-22 “Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzisintha Ulaliki Wanu