OWERUZA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Madera omwe Yuda ndi Simiyoni anagonjetsa (1-20)
Ayebusi anapitiriza kukhala ku Yerusalemu (21)
Yosefe anagonjetsa Beteli (22-26)
Akanani ena anasiyidwa (27-36)
2
3
Yehova anayesa Aisiraeli (1-6)
Otiniyeli, woweruza woyamba (7-11)
Woweruza Ehudi anapha mfumu yonenepa Egiloni (12-30)
Woweruza Samagara (31)
4
Mfumu Yabini ya ku Kanani inkapondereza Aisiraeli (1-3)
Mneneri wamkazi Debora ndi woweruza Baraki (4-16)
Yaeli anapha Sisera mkulu wa asilikali (17-24)
5
6
Amidiyani ankapondereza Aisiraeli (1-10)
Mngelo anatsimikizira woweruza Gidiyoni kuti amuthandiza (11-24)
Gidiyoni anagwetsa guwa lansembe la Baala (25-32)
Mzimu wa Mulungu unathandiza Gidiyoni (33-35)
Kuyesa ndi ubweya wa nkhosa (36-40)
7
8
Amuna a ku Efuraimu anakangana ndi Gidiyoni (1-3)
Mafumu a ku Midiyani anathamangitsidwa nʼkuphedwa (4-21)
Gidiyoni anakana ufumu (22-27)
Mbiri ya Gidiyoni (28-35)
9
Abimeleki anakhala mfumu ku Sekemu (1-6)
Mwambi wa Yotamu (7-21)
Ulamuliro wankhanza wa Abimeleki (22-33)
Abimeleki anapha anthu ku Sekemu (34-49)
Mzimayi anavulaza Abimeleki ndipo anafa (50-57)
10
Oweruza Tola ndi Yaeli (1-5)
Aisiraeli anasiya Mulungu kenako nʼkulapa (6-16)
Aamoni anaopseza Aisiraeli (17, 18)
11
Woweruza Yefita anathamangitsidwa kenako anakhala mtsogoleri (1-11)
Yefita anakambirana ndi Aamoni (12-28)
Lonjezo la Yefita komanso mwana wake wamkazi (29-40)
12
13
14
Woweruza Samisoni ankafuna mkazi wa Chifilisiti (1-4)
Mzimu wa Yehova unathandiza Samisoni kupha mkango (5-9)
Mwambi wa Samisoni pa ukwati (10-19)
Mkazi wa Samisoni anaperekedwa kwa mwamuna wina (20)
15
16
17
18
19
20
21